25/08/2026
Ati "atsikanawa akundithera zitenje zanga" agulireni zawo. Mwana wankazi azikhala ndi zitenje ziwiri.
It begins with us mothers!
Komanso anzathu mumasoketsa aja taonanipo apa, nsalu zotchenela bwino izi.
Tikuti K6,500 basi. Wax wa quality yabwino.
We are along Midima road, pafupi ndi weaving factory and opposite Bangwe Evangelical church. Timatumiza kulikonse.
0888757395
0995434520
Zikomo!