08/07/2026
Anthu a ku Bangwe, Namiyango, Chigumula, Kachere, Makheta ndi madela Ena ozungulira, Kuli mwai wa ntchito.
Sentinel Guard Services ikufuna Anyamata ndi Atsikana oti atha kugwira ntchito ya chitetezo (Security Officers) ku Malo osiyanasiyana.
Zokuyenerezani,
1. Mukhale nzika za dziko LA Malawi (National ID)
2. Mukhale ndi JCE kumakwera
3. Mukhale oti mumamva ndi kulemba komanso kuwerenga chizungu
4. Mukhale ndi mbiri yabwino (Okuba uku ayi)
5. Mukhale okonzeka kugwira ntchito nthawi iliyonse kuohatikizapo usiku.
Amene mungakonde kapena m'bale wanu akufuna ntchito, imbani phone pa number izi kuti mumve zambili
0897 66 93 31 kapena 0991467764