20/06/2026
&in all fairness don't be cheated boys,kusachita bwino kwa flames it's not about kuti ma players ena anapanga misbehave nde anasiyidwa,i know zikhoza kupanga affect inde but ma coach athu ndi omwe akuthandzira team kusachita bwino.
Aliyese amaona zomwe zimachitika,or ma player abwino atengedwe,ma game ena mumaona zomwe amalowetsa mkuluyu, you want to tell me kuti muja amachitira Malango Mayele muja angamamulowetse kwatsala less than 6 minutes in several games? and you expecting team to win? in all fairness you want to tell me pali dzuwapa kuti Yankho Singo is better than Blessings Singini? but check the statistics,muona Singo wagalauza ochuluka ku flames than singini,komatu Singini amakhala watengedwa,and akalowa Singiniyo mumaona zomwe amapanga.
Let me tell you anthu mumanena kuti Flames or kutabwera Arteta palibe chomwe ingachite, yeah it's true chifukwa even Arteta atapita ku converntry City muona ngati angatenge league? success ya team it's about achieving zinthu zomwe ena amaganiza atalawa kam'pwanthi noo, moving from step 1 to step 2 nd success kale imeneyo, malawi ili ndima team a size yake,ndipo ndukuuzani kukhala ndi coach oganiza boh,or osatenga ma player akuti amapititsa akazi ku camp-wo Malawi ikhoza kumawina against ma team ngati Botswana, Ethiopia, Tanzania, Zimbabwe, Zambia, Mozambique, Uganda, tikhoza kuwina ndukuuzan, awaa ndima team a level Yathu, once team ikukanika kumawina against tima national team ndakambati nde muti tikawina atiwo?mudziwe kuti coach uyu ntchito yamuvuta.
Ndikuuzen, mkuluyu simmadana nayetu,but i have experience pa mmene amagwilira ntchito especially on international matches, even ku Bullets mipira ya international imamuvuta kuwerenga, mukhoza kuona game yomwe Bullets inatuluka ndi Amazulu after claim a 1_0 victory away from home,zinachita kuonekeratu kuti mdalayu game plan pa international level mulije, Bullets kufa nd FC platinum ku Zimbabwe game inachita kuonekeratu kuti mdalayu game plan mulije pa international level,
mwina muona ngati ndaledzera,ayi ndithu, akanakhala kuti nd Coach wanzeru believe me Bullets sikanatuluka nd red arrows ku Zambia,zinachita kuonekeratu kuti mdalayu pa international level ziganizo zimamuvuta kupanga
Inuyo kaya mundithira maphuzo,zanuu,koma dziwani kuti flames ili ndma team a size yake omwe ikhoza kuwagonjetsa,so ngati sitikuwina ma game ngati amenewo muti tikawina atiwo? And tell me muti vuto Mndani?..
Ndima player omwewa omwe timawina nawo ma game ena tikawalowetsa mwanzeru,but now tikuoneka tikuyenda chobwelera mmbuyo
Vuto chilungamo ndi mwanotu, chilungamo changa sindingabise,amadana nacho kwambiri ndi mapale,i know this guy anagwira ntchito yotamandika kubanja lanu during his time koma zimenezo sizingapange block ineyo kunena chilungamo zokhudzana nd national team, coach uyuyu sangatithandize,nokha mukuona zomwe anapanga nd Bullets mu CAF, zikuchitika kuonekeratu kuti pa international level uyu ziganizo zimamuvuta kupanga.
& I don't know kuti ku FAM Mndani anayambitsa motion yoti Pasuwa alembedwe ntchito yet anali nd season yoyipa kwambiri yomwe anaonekera ng'amba kuti mdalayu amadalira Chatama after rerseve ya Chatama kutsika mphavu? How come ntchito kukapatsa munthu amene anali nd season yoyipa and Bullets imkafuna kumuchotsa ntchito mpaka?😴🤐
Pangani register on 1WIN using promo code Abel1 Link ??
https://one-vv9031.life/
Zikavuta contact me on wapp
0882929305 ndikuthandzan↘️🎙️