Traver Mw

Traver Mw Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Traver Mw, Food & Drink, traverjohn772@gmail. com, .

30/03/2026

Eti ndizoona ukagwira Lamba wachigayo chikulira Chimazima?🧘🏾‍♂

30/03/2026

Kupatula

1: Usalonze kumanda chala chimapindika
2: Osaliza likhwelu madzulo njoka zimabwera

3: osaseweretsa moto madzulo afiti amakuona ndipo amapanga zaiwe

4: osayenda opanda malaya Chifukwa afiti amakuwerenga mthiti

5: Ukatseka maso ako mwachangu ndik*tsegulaso pakamwa ukupapotoza amati ndik*tukwana😂😂

Zina ndiziti tikumbutseni zomwe makolo amkatinaminza karelo 😂😂

30/03/2026

💖 A GIRL WHO REALLY LOVE ME 💖

💥 PART 3 💥

PANGANI LIKE , COMMENT AND SHARE NKHANI ZATHU NDIZAULERE AMZANU AMVE NAWO KUKOMA NDITHU

Apa fro adali atalowa mkalasi tsopano

fro: wow ukuoneka smart yami

yami : zikomo kwambiri fro sindikudziwa k*ti ndik*thokonze bwanji ?

Fro : noooo ndine mzako yami vuto lako ndilangaso limenero osadanda

mike : ayami nkhani ndiyomwe ijatu eti

fro : kod umakambirana nawo chani amenewo ?

Yami : aaaaaaaa asiye paja machenza awo sakhala abwino kwaine

apatu mmene imati 7:30 nthawi yamma class ndipomwe achina tiwonge amatulukira

tiwonge : heeeeee ayami kungobwera mkaziyu mwasinthatu ndiyesa mwampangira makhwala abare mukuona koma

takondwa : eeeeeeh yami ndi iweyodi ?

Apatu yami amkamuyang'ana takondwayo

takondwa : mwaoneka bwinotu ngati sinu wakare uja odi ndikakhale kumbuyo

iyi idali mbali imodzi yomwe yami adayamba kupenzano azimzake pa xul pa

apa takondwa adayamba kuchenza ndi yami tsiku limeneli

takondwa : fro and yami sorry pot ndakhala nthawi yayitali mdani wanu koma ndikufuna mundikhululukire

apatu yami adamwetulira navomera apatu adayamba kuchenza komano azimzake a takondwa aja sadali kukondwa nazo zinthu ngati izi .

matsiku adapita ndipo tsiku lina adawapatsa test kufuna kuwayetsa ngati alindi mzeru ana a form 3 ndipo italembedwa zidapenzeka k*ti yami adalakwa koma fro adakhonza number 1 izitu fro sizinamusangalatse komaso takondwa ndipo tsiku ili silidali labwino kwaiwowo apatu fro ndi takondwa adangwirixana k*ti azisalira kumuthandizila yami nkhani ya xul ndipo zinayamba kuchitikadi koma nthawi zambir amasalira ndi yami ndi fro bas takondwa nthaw zambir amakhala wauletsi ndipo yami adazitolera mzeru zake zonse mpaka adayamba kuchita bwino.

tsiku lina fro adamutsadzika yami k*t akukamwa kaye madzi ndipo uku adakumanako ndi mike ndipo zinali chomchi

mike : hy fro

fro : yes

mike : sorry pazomwe ndimkachita

fro : its oky

mike : kodi ungandikonde ?

Wait 3b 💖💖💖 A GIRL WHO

30/03/2026

💖 A GIRL WHO REALLY LOVE ME 💖

💥PART 2B 💥

ndalama yokwana 8thousand yomwe adapatsidwa ngati yodyera yake patsikuli adamupatsa yami ndalamayo ndikumuwudza k*ti akagule soap ndipo akachape akaweluka komaso akagule timafuta tozola

apatu yami adakana kulandira ndalama ija ndipo adalimbana kaye k*t avomere ndipo zinatero adazungulira ground ija kenako belu idalira yokalowera mkalasi ndipo onse adalowa mkuyamba kuphunzira ndipo nthawi yowelukila itakwana kudatulukila galimoto yomwe idabwera kuzamutenga fro , uyutu adali wantchito amane amazamutenga ndikuzamusiya fro ku xul ndipo apa fro adamuwudza yami k*ti apitile limodzi akamusiya kwawo ndipo apa adakweradi kenako ulendo 🚙 .

atafika pafupi ndipakwa yami adatsika apatu fro adamukumbatsa yami za soap komaso mafuta ndipo izi adakumbukila apa galimito ija idabwerela mkumapita kwao fro

Apa yami atafika kwao adali wamafunso kwambiri k*ti mchifukwa chani mkazi uja sadamumve fungo lake ndipo adawapenza agogo ake akugona

adaphika nsima mkuwapatsa agogo ake aja ndipo adapita pa shop kukagula soap ndi mafuta aja apatu adachapa zovala zija ndipo zinayera

💥NEXT DAY MORNING

Apatu a yami adavala zovala zoyera ulendo ku xul ndipo atalowa anthu adali odabwa

mike : aaaaaaa iwe aise wakusambitsa ndindani lero kumanenatu k*ti mwalowa satanic nafeso tikalowe nawo nanga maloza anji omwe tikuona lerowa ?

Ndipo class yonse idaseka

apatu yami adaona k*t fro sadabwere adakakhala pamalo pake paja ndikumadikila k*t fro abwere

Posakhalitsa mzake wa mike adalowa uyutu adali jue

mike : a jue lero kugwa mvula man

jue : bwanji ???

Mike : iiiiiiiii atobias aja lero avala zoyeratu 😂😂

Apa jue adayang'ana kumbuyo mkuyamba kuseka 😂😂

Jue : eeeeeeeh ayami kungomva k*ti chidanenepetsa nkhumba sichidziwika ndiye mwati ndi inuso ? Aaaaaaaa koma udyera

Wait 2C

Sorry nkhaniyi ndayilemba yayitali koma ndikafuna kuvunga kuno ikumadula mutikhululukirako💖 A GIRL WHO REALLY LOVE ME 💖

💥PART 2B

30/03/2026

Azimayi si anthu omawatengera, olo popita kumalilo amatha kugwirizana kt kulila tikayambire pansewu paja.
ndi achibwana 😂😂

30/03/2026

💖A GIRL WHO REALLY LOVE ME 💖

💥PART 2💥

Apatu tiwonge amayankhula uku akumuyang'ana yami moyipidwa

Yami : Tiwo tipatsanepo ulemu bwanji ?

Tiwo: ndikakupatse ulemu munthu onukha ngati iwe ? Azikupatsa ulemu ndi amene akubwerayo osati ine .

Apatu fro adafika pamene padali yami paja ndipo zinali motere

yami: sorry msikana sukuyenera kukhala ndi ine malingana ndimmene ndiliri

fro : mmmmm ak*tero ndindani k*ti aindikuyenera kukhala nawe ? Usadandaule zaine ingondipatsa malo

Apa yami adamupatsadi malo fro k*ti akatopa ndi fungo lakero achokapo yekha komatu zinali zodabwitsa mpaka adafika nthawi ya break.

Anyamata a class iyi adali adabwa kumuona mkaziyo owoneka bwino ngat ameneyu akukhala ndi mamuna ochititsa nyasi ngati ameneyu ( yami )

Class mo mudali mike : uyy adali mnyamata amene amadziwa kuvala zovara zapamwamba ndipo adali ozifila pa xul ponse k*t iyeyu palibeso ndipo asikana amamufila malingana ndimavalidwe komaso maonekedwe ake ndipo atamuona fro pa break alind yamibe adapita pomwepo

mike : Achina lomeo ndi juliet aulendo uno kodi eti ? Komaso mkazi kodi umadwara vuto la mphuno eti ?

Fro : ayi bwanji wafunsa ?

Mike : haaaaaa tiziti sukumva ka perfume ka adha wakhala nawowo ? Kodi ?

Fro : sorry kod vuto lanu ndi chani anthu inu ?

Apatu fro adamupempha yami k*t atulukeko panja akamuonetse malire a xul yawoyo

koma yami panthawi iyi adali omangika kwambir ndipo adatulukadi ndipo akuyenda adayamba kuchenza ndipo zinali motere

fro: oooook sindingakufutse dzina lako pot anthu ambiri amalitchula class muja ine ndi frolida utha kumangot fro , oky yami pls ungandiwudzeko background yakwanu ?

Apatu yami adafotokonza mmene adakulira ndimavuto ake kufikila makolo ake atamwalira k*tsara ndi agogo ake .

ndipo izi fro zinamukhunza mkulingaliraso ndimmene anthu amamunenera komaso kumuthawira mkalasi muja ndipo adamuyang'ana yami uniform yake idali yakuda kwambiri apatu fro adatulutsa ndalama yokwana 8thousand

Wait 2B💖A GIRL WHO

30/03/2026

💖 A GIRL WHO REALLY LOVE ME 💖

💥PART 1 💥

Nkhani iyi ikukamba zamamuna amene adali osauka ndipo even ku xul anthu amamusala , koma chipite chanthawi pa xul po padabwera mpulumisi mumoyo mwake mkuyamba kumvana naye injoyeni 💗💗🙃

Ndinabadwa poti anthu amabadwa ndipo ndikukhala poti anthu amakhala , dzina langa ndine yamikani makolo anga adamwalira kale kale ndilindi zaka zochepa nthawi imeneyo ndipo pano ndimakhala nd agogo anga mmoyo ongoti bora tilimoyo

💖Monday morning 💖
Yami adali kukonzeka k*t azipita ku xul koma kamba k**a busy sakanakwanitsabe kumapita mwachangu ku xul chifukwa zinthu zambiri zimayimira iyeyo agogo ake sakadatha kupanga chilichonse k*tengera zaka zawo ndipo yami nthawi zambir amachedwa .

Go!! Go!! Go!!
Uyu adali yami kugogoda mkalasi k*ti alowe apa nthawi idali ili past 9 adali akuchokera kwawo .

sir : you again ? Kod ngat xul ikuvuta bwanji osangosiya ? Wandikwanatu tsopano sukuyenera mkalasi mwanga iwe !!!!!! Bwalera uzabwere mmawa mwachangu k*ti uzalowe priod yanga .

Apatu yami adapepesa ndikupempha sir uja ndipo adamupatsa chibalo ngati chilango .

Tikanena kumbali ya yami sadali ozisamalira pathupi pake kotero or class iyeyo amakhala payekha anthu amamuthawa chifukwa amatulutsa fungo lomwe anthu amadana nalo chifukwa chakusasamba , uku kudali kusowa chithandizo kwa yami .

TAKONDWA
TIWONGE
TRISHA

Awa ndi atsikana omwe adali kumuda kwambir yami .

Takondwa : mmmmmm bodza kunena mosanama mamuna uyu amandinyasa sindifuna kumuonaso 😩

Apatu yami adali akupita pamalo pake

Tiwonge: ndipo or inesotu amandipatsa mseru haaaa!!!!

Trisha : Ubwino wake sachenza ndi ife ndi fungo lake lakuchimbuzilo asikana tiyen tikakhale k*tsogolo

Mmene amateromu enaso omuyandikila adali akupitaso k*tsogolo k*thawa fungo la yami .

moyo wa yami udali ovuta kwambiri k*tsalidwa ndilo gwero lalikulu pamaphunziro ake , mkalasi samachita bwino amakhala omalinza kwa olakwa mak**aka mayeso akalembedwa

wait💖 A GIR

30/03/2026

🌚 😂
(||\_🔑 _/||)
/ \. / \
Man katundu wanu uyu mkazi uja ATI sanakonzeke😩🙄

30/03/2026

Kusiya K5000 pobwera ndapeza waphika Bonya kenako ndazasiya 2 pin ndikupeza wagulaso Bonya
Siku lina ndasiya 8000 pobwera ndapedza Soya Pieces ndi nkhwani.
Kenako ndati ndifuse kodi ma program anu andiwo mukuwakonza motani

Eeesh nde ndapalamulatu ati uona ngati ndimakubera ndalama zako? Kuyambila lero usazandipaseso ndalama zako. Uzigula zonse wekha uk**abwera moti pano akungokwiya.
Nditani pamenepa?

30/03/2026

NDUDU YA KINGS K200
NJERWA K50 ,
WINAWE NDE UNASUTATU CHI MASHON 😂

30/03/2026

Ndamulowesa m'nyumba mozemba🙎
Ndat ndkamugulire fanta pobwera
Ndapeza akuwathandza amayi anga
Kuwatukwana aneba🙆🙌🙄

30/03/2026

Et chizungu cha k*thawa mimba ndi chan🤨 ???

🏃🏃🏃🙆

Address

Traverjohn772@gmail. Com

TRAVER

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Traver Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Food & Beverage Service?

Share