31/10/2025
oyenda ndi yesu sachita mantha or adani atachuluka motan mulungu azakumenyera nkhondo iwe uli chete YOHANE 3 :16 pakuti mulungu anakonda dziko lapansi kutelo anapeleka mwana wake obadwa yekha kuti onse onkhulupilila iye asatayike koma kuti akakhare nawo moyo osantha .