Tatiya Foods and General Dealers

Tatiya Foods and General Dealers Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tatiya Foods and General Dealers, Food Wholesaler, Area 25, sector 4, Lilongwe.

Welcome to Tatiya Foods & General Dealers! 👨🏽‍🍳🐓🐟🍽️ ✨Your one-stop-shop for:
✅Food production & Food Processing
✅ Poultry
✅Aquaculture
Follow us for updates, tips, and mouth-watering deals!
🚨(Authorised CP Feeds distributor)🚨

Zinali motere tikutseka gulu lomwe linazaphuzila nawo class ya march kuno Ku Tatiya🥳. Kuphuzitsidwa ma luso osiyana siya...
15/03/2025

Zinali motere tikutseka gulu lomwe linazaphuzila nawo class ya march kuno Ku Tatiya🥳. Kuphuzitsidwa ma luso osiyana siyana monga kuphika zakudya za chikhalidwe chathu chachi Malawi, zakudya za mayiko ena🌎, Kusamala Khomo komaso kupanga Ma cake🎂🧁🍰, monga mwa zina zochepa🌝. Registration ya April, yayamba kale azimayi ndi abambo, tosangoti manja lende bwerani tiphunzire luso kuti moyowu uzisuntha.🥳🥳

Happy Valentine's Day Lovies❤️Sizoti next Valentine's muzapiteso pa chiwaya😂 pa 1 March school yazophika and home manage...
14/02/2025

Happy Valentine's Day Lovies❤️

Sizoti next Valentine's muzapiteso pa chiwaya😂 pa 1 March school yazophika and home management ikuyambatu paja, let's register fast fast.😚

🚨Tiyeni tizidziwa mitundu ya anyezi, makomedwe ake komanso kagwilitsidwe nchito kake ..osangoti bola ali anyezi💯🎉Anyezi ...
05/02/2025

🚨Tiyeni tizidziwa mitundu ya anyezi, makomedwe ake komanso kagwilitsidwe nchito kake ..osangoti bola ali anyezi💯🎉

Anyezi alipo oposela mitundu 25 ndipo aliyense amanveka makomedwe akeake.Tizimunvetsela anyezi makomedwe osangoti bola wanunkhila 🥰
Koma kwalero, tikhala tikuona mitundu yochepa chabe.

‼️PAJATU School tikuyamba pompano, 1 March ma class tikutsegula...Bwerani tiphuzile limodzi🥳🥳💯

Kamtengo pang'ono, LUSO lambiri 🫶🏽Ma class akuyamba pa 🗓️ 1 March, pangani register mwachangu.✅
25/01/2025

Kamtengo pang'ono, LUSO lambiri 🫶🏽

Ma class akuyamba pa 🗓️ 1 March, pangani register mwachangu.✅

😶‍🌫️Koditu ma cake tima baker so akasi🌝👨🏽‍🍳Ma cake a mitundu yosiyanasiyana:  Red velvet cake, Carrot cake, chocolate ca...
23/01/2025

😶‍🌫️Koditu ma cake tima baker so akasi🌝

👨🏽‍🍳Ma cake a mitundu yosiyanasiyana: Red velvet cake, Carrot cake, chocolate cake, Banana Cake and sweet potato cakes. Nkhani NDI yomwe inetu, lembetsani Kuti mukhale nawo limodzi pama class omwe akuyamba pa 1 March Kuti muzathe kuphuzila nawo. Nanu mukhale ozitsata🥳🥳

Registration is still in progress...anawo atsekela Koma asamangokhala pakhomo, abweretseni kuno tiwaphunzitse kuphika nd...
21/01/2025

Registration is still in progress...anawo atsekela Koma asamangokhala pakhomo, abweretseni kuno tiwaphunzitse kuphika ndi kusamala pakhomo🌝

🤔Looking to upgrade your Cooking skills, Baking skills, Home management skills? Worry not, Tatiya has you covered.🫂

✅Join Us today and be part of our first cohort this year starting on 1 March 2025, Luso loyambila Business tu ili akasi.😉😉

Today, we Celebrate the life of one of the iconic figures in Malawian History, your legacy lives on Reverend.🫡🇲🇼
15/01/2025

Today, we Celebrate the life of one of the iconic figures in Malawian History, your legacy lives on Reverend.🫡🇲🇼

SAUSAGE ROLLS🌭🌭INGREDIENTS1 Cup Milk2 eggs1/4 cup Sugar2 Instant yeastpinch salt2 tbs Butter6 Sausages2 cups of Flour Th...
14/01/2025

SAUSAGE ROLLS🌭🌭

INGREDIENTS

1 Cup Milk
2 eggs
1/4 cup Sugar
2 Instant yeast
pinch salt
2 tbs Butter
6 Sausages
2 cups of Flour

The process:

✅Mix milk and eggs, stir well.
✅..Mix the other ingredients
✅After that kneed the dough until smooth and soft then cover again
✅Then let it kuti ifufume(20 to 25 in a mild hot temperature)
✅Then tiyeni tipange roll mmene tipangira chapati.
✅Sausage yathu tingophika pqngono kuti iphye nkati
✅Tipange roll to make them flat...then put sausage on middle...take a cutter and start cutting the dough next to sausage.
✅Kenako kuyamba kuluka ngati mesh
✅Then brush with beaten egg...
✅Now...you can bake as it is or put sesame seeds

We can do sausage rolls of different shapes❗. Bwerani tikuphuzitseni kuno Ku Tatiya, classes start on 1 March 2025.❤️🔥

🤔Looking to upgrade your Cooking skills, Baking skills, Home management skills? Worry not, Tatiya has you covered.🫂✅Join...
13/01/2025

🤔Looking to upgrade your Cooking skills, Baking skills, Home management skills? Worry not, Tatiya has you covered.🫂

✅Join Us today and be part of our first cohort this year starting on 1 March 2025, Luso loyambila Business tu ili akasi.😉😉

Join Tatiya Cooking School's upcoming program, starting March 1st, 2025!❤️Gain skills, confidence & expertise to succeed...
09/01/2025

Join Tatiya Cooking School's upcoming program, starting March 1st, 2025!❤️
Gain skills, confidence & expertise to succeed in the culinary world!
ENROLL NOW! 🎉🎉

Address

Area 25, Sector 4
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tatiya Foods and General Dealers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share