19/02/2026
Mklu ameneyu ndi JB zikumveva kuti akufuna ku joiner MCP wamutulika muthalika, malangizo kupita kwa JB chakwera sanaiwale kuti unkamunena ma battery ndipo kinena mwachidule zilingati wabiba ku toilet kenako ukupita kukasetela mtengo wa kankhande kunkhalango Mr JB musaiwale kuti MCP simapanganika kumvukilani chilima zimene anamupanga, komanso wina aliyese amene amati akanyoza chikangawa party kenako ndikujoina amaphedwa, zikuoneka kuti JB ukufuna pofela, amati pofera salambula koma JB walambula