Timphunzisani maphikidwe AMAYI

Timphunzisani maphikidwe AMAYI Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Timphunzisani maphikidwe AMAYI, Food stall, 149, Mzuzu.

29/03/2025

muli bwanj azimai pa group pano ya za maphikidw?

29/03/2025

Moni nonse ndikufuna mundiphunzise kumphika makeke I

15/02/2025

Guys Kodi cake ndinga bake bwanj?

07/02/2025

Tilibwanji tonse pano alipo akufuna kukhala admin muno

17/11/2024

mwaswela bwanji abale ndi alongo

06/11/2024

Tiphunzitseko kaphikidwe ka pizza alipo amatha kuphika pizza atiphunzise please

24/08/2024

kodi sausage wa soya pieces amaphik bwanji

17/04/2024

Kodi madonas amaphika bwanji azimay

17/04/2024

Ndapanga group pa wap anthu omwe akufuna tiwapange add pelekani ma number

16/04/2024

Inetu basi azimayi chigumu mundiphunzisa kuphika chija ndinayesela ndipo chinakoma ndipo ndende ngati bread ndikuoneseni eti

16/04/2024

Kwacha bwanj mmadelamu

13/04/2024

Kd mandasi oyikamo yeast umaikaso mazira nd mkaka morning

Address

149
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Timphunzisani maphikidwe AMAYI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category