GOH

GOH Healthy

19/09/2026

tikhala tikuwanenera anthu pano. kaya ndizizinenera ndekha nthawi Zina ndiziziwa ndekha.

19/09/2026

anenele sakukondwa nawo. ine ndiwanenerebe basi sitikufooka

19/09/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Dennis Mapesah, No Bady Boy

18/09/2026

Any way pamene tili pakatikati posova ubale wanga ndi akabanza nditakonzanso ubale wabwino ndi company ya Sophi. kaya Blantyre kaya. Rab Processors Kanengo NKHANI ndiyomweyija osayiwala kupanga process ND tomato emwe komanso mafuta. needy wadandaula kuno. nyimbo ndiyomweyija mkasa anenere sakukondwa nawo.

18/09/2026

company ya Sophi

14/09/2026

ndati ndikusimikizileni abale ndi alongo.

nyashi ija izapititsa ww moyo ndithu

14/09/2026

Kodi NKHANI iyi mwayifila? dinani more


Nkhan Yosangalasa Pokudya Nsima. MWANA; AnafuNsa.... Adadi Mkazi Munali Naye Patchile Uja Ndndan? ABAMBO.... Shatap!!! Sitimaykhula Pokudya Nsima.. AMAYI.. Iwe Umati Unawaona Bambo Ako Ali Ndimkazi Patchile Amatanipo? MWANA;. Anayankha Amachta Zija Mumachita Ndi Aneba Kuchipinda Adadi Akachokapo Zija... AMAYI; Shiii!! Paja Bambo Ako Anati Sitimaykhula Pokudya Nsima.

Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

anyamata aja ndi amenewa omwe akumapepetusamo nthinti  yanga kufuna kuthawitsa  mdima ufika bho bho tikumana nawo tiwawo...
11/09/2026

anyamata aja ndi amenewa omwe akumapepetusamo nthinti yanga kufuna kuthawitsa mdima ufika bho bho tikumana nawo tiwawonetsa

09/09/2026

paja akabanza akumakonda kuthawa ndi thinti zanga. ndawagulira raincoat izinyethima azindisokoneza ndi akabanza anzawo. koma ndizilibvumbulutsa khofi magesi akangothima

08/09/2026

wakabaza kuthawitsa nthiti

Address

ENOCH MANDALA
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GOH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share