Faith wa Flynn

  • Home
  • Faith wa Flynn

Faith wa Flynn Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Faith wa Flynn, Grocers, Lilongwe, Malawi, .
(1)

Pa birthday yanga muzabwera kuzadya nawo khekhe kapena zopusa mumadana nazo?? 🤣🤣🙌
11/06/2026

Pa birthday yanga muzabwera kuzadya nawo khekhe kapena zopusa mumadana nazo?? 🤣🤣🙌

10/06/2026

Mutani nthawi zino pa line?
🤗🥱

Kodi Nanuso mafuta amphamvu Hair Food mukuwafuna koma ndalama mulibe kae, lowani nawo mu challenge iyi imene ithe mawa 8...
09/06/2026

Kodi Nanuso mafuta amphamvu Hair Food mukuwafuna koma ndalama mulibe kae, lowani nawo mu challenge iyi imene ithe mawa 8am.

Amene ataike comment imene pofika mawa 8am sikhala ndi like azalandila mafutawa botolo limodzi la ulere. Invite your friends mwina nawo mkuchita mwai

Osayiwalaso kuti mukagula mabotolo teni, muzapatsidwa botolo limodzi la ulere 👏

Gulani mafuta okulitsa tsitsi, kuchosa, mfundu, zipele, zikanga, kuletsa kuyabwa ndi kuthothoka kwa tsitsi, azanutu akusimba lokoma nanga inu mukuchedwa pati?

Halla WhatsApp or call 0891142406 tili mu Blantyre limbe, soche or tikumane mu Blantyre town pakandodo & panandozi.

MPHAVU HAIR FOOD100grams
1 Bottle k12000
2 bottles k24000
3 bottles k36000
Pa order 👇👇
5 bottles k45000
10 bottles k90000

250grams
1 bottle k25,000
2 bottles k50,000
Order
5 bottles k90,000

Okondedwa makolo tikukuitanani ku kids festival yomwe izachitike pa 5 July 2026, venue ndikwa ntawale near Mapale hospit...
09/06/2026

Okondedwa makolo tikukuitanani ku kids festival yomwe izachitike pa 5 July 2026, venue ndikwa ntawale near Mapale hospital, tawabweletseni ana anuwo kuti tizasangalale limodzi patsikuli, ukutu tikufuna ana oyambila zaka ziwiri kupita mtsogolo.

Inuso makolo bwelani bwelani muzawajambule ana anu akusangalala ndi masewera osiyasiyan ndipo simuzakhumudwa ayi

Ukutu kukakhala phwando losayiwalika ndipo ngati mukufuna kudziwa zambiri tipezeni pa number yathu iyi +265998886141

Thank you so much ❤️
08/06/2026

Thank you so much ❤️

06/06/2026

Atchena alexina kuno 😂😂🙌

06/06/2026

Koma zagwirizana pati 😂😂🙌

05/06/2026

Ayiwala chimene anabwelera 😂😂🙌

Wina mawa andipelekeze kwa Luwinga opposite rank yama lorry Tikagule dining set ndi bed la FlynnAwa amapezeka ndi Katund...
04/06/2026

Wina mawa andipelekeze kwa Luwinga opposite rank yama lorry Tikagule dining set ndi bed la Flynn

Awa amapezeka ndi Katundu Olimba ndi wa quality, lay by amaloraso bwino bwino 🔉

Hi Mrs fly p , I hope your doing great....post this for me, am looking for a young lady amene alibe zochita akhale oti a...
04/06/2026

Hi Mrs fly p , I hope your doing great....post this for me, am looking for a young lady amene alibe zochita akhale oti amatha kumanga tsitsi azayambe ntchito anyday

Koma akhare around chibavi , mchengautuba ndi bishop, za salary tizamvana ku inbox akandihala.

My number +265982451437

Address

Lilongwe, Malawi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Faith wa Flynn posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Food & Beverage Service?

Share