14/10/2026
π₯ 17 BORN. 16 WEANED! Good Genetics, Proper Nutrition & Good Management!
Ana 17. Tapanga wean 16! π Kodi ichi chikutiphunzitsa chiyani pa ulimi wa nkhumba?
On 1 September, this sow gave birth to 17 piglets. By 12 October, 16 piglets had been successfully weaned at just 6 weeks of age! πͺ
Ku MAAG FARMS, timakhulupirira kuti ulimi wa nkhumba wopindulitsa umayambira pa zinthu zitatu zofunika:
β
Good Genetics | Mitundu Yabwino: Choosing quality breeding stock with the potential for good performance.
β
Proper Nutrition | Chakudya Choyenera: Kupereka chakudya chopatsa thanzi komanso chosakanizidwa moyenera, kuphatikizapo kugwiritsa ntchito U-MIX macropacks.
β
Good Management | Kasamalidwe Kabwino: Monitoring the sow's body condition, ensuring adequate nutrition during lactation, and providing proper care for both the sow and her piglets.
π Farmer's Lesson | Phunziro kwa Alimi
Look closely at the sow in this picture. Nursing a large litter requires a lot of energy. Proper feeding is essential to support milk production and minimise excessive loss of body condition.
Yang'anani bwino nkhumba ya pa chithunzichi! Kuyamwitsa ana ambiri kumafuna mphamvu zambiri. Choncho, chakudya chokwanira komanso chopatsa thanzi n'chofunika kuti nkhumba ipange mkaka wokwanira komanso isawonde mopitirira muyeso.
At MAAG FARMS, we put good genetics, the right nutrition and sound management into practice. We believe in sharing real farming experiences to help farmers improve their productivity and profitability.
Ku MAAG FARMS, sitimangolankhula za ulimi. Timagawana zomwe timachita komanso zomwe timaphunzira kuti alimi ena apindule!
π· Looking for quality breeding stock? Contact MAAG FARMS today!
WHERE CAN YOU GET U-MIX FOR PIGS?
π° U-MIX for Pigs β MK42,500 per 3kg pack only at MAAG FARMS.
π Lilongwe: You can now get your UMIX macropacks at Crossroads.
π Call: 0999957417
π Mzuzu: Call this number(Mchengawutuwa) :0884265767
π Blantyre & Nationwide:
π Call: 0888764048 / 0881922370 / 0881254009
π± Tiyeni tiphunzire. Tiyeni tiwete mwanzeru. Tiyeni tipange phindu.
Follow our MAAG FARM Page for insights, tips and updates