Zanthu zomwe

Zanthu zomwe Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zanthu zomwe, Grocers, Blantyre.

10/10/2024

Nditapita Kuchipatala Chifukwa Cha Mavuto Ena, Adotolo Anandiuza Kuti Ndisiye Kumwa Mowa..Koma Nditawaunikira Za Ubwino Ndi Kukoma Kwa Mowa ,Adotolowoo Anati M'bale wanga Kapitilize ...Ndipo Pano Naye Wayamba Kumwa. πŸƒ

Today was supposed to be their wedding anniversary.  May God comfort Madam Mary Chilima πŸ™
29/09/2024

Today was supposed to be their wedding anniversary. May God comfort Madam Mary Chilima πŸ™

Madam Mary Chilima lero angozuka ndikusitha maganizo awo pa za Imfa ya SKC, mbuyomu amakhala ngati amavomereza kuti inal...
29/09/2024

Madam Mary Chilima lero angozuka ndikusitha maganizo awo pa za Imfa ya SKC, mbuyomu amakhala ngati amavomereza kuti inali ngozi koma lero akufunanso kafukufuku wina wapadera

Ndadzuka wa mantha komaso wozizidwa nditaona chithunzi ichi πŸ’”πŸ˜­

Mayi Mary Chilima akundimvesa chisoni πŸ’” , mayi uyu wavutika kwambiri mumtima ndipo akumva ululu kwambiri mmoyo mwake. Mayi mwina ndiyese ndikaona mtengo akuti udapha amuna anga Biyeni koma mayankho osapezeka.

Kodi nchiyani chomwe woyipayo adalephera kukhululuka mpaka zongoganiza kuti Chilima asadzapezekeso padziko ndi anthu ena asanu ndi atatu ? Zikumatizunguza mutu a Malawi ndithu. Lero mabanja oferedwa ali khumakhuma chifukwa achibale awo adathera ku Chikangawa ati ka mtengo ndikomwe kadakola Ndege ija πŸ˜­πŸ’”.

Anthu inu simudapite bwino a Malawi zikutivuta kuyiwala ndipo wina kaamba akudya chibanzi chothira msinjiro akumalankhula mwathamo kumati aliyense adzafa lekani kukamba nkhani za Chilima komaso osalowetsapo ndale pa za ngozi imeneyi. Ali m'bale wako wina wapita chotere wina mkumakuuza kuti aliyense adzafa iwe ungamve bwanji? Andale kaya si andale akukamba nkhani ya Chilima chifukwa adali wa ndale ndipo wamwalira ali wandale. Iwe yemwe udachita izi uzigugude pa mtima ndipo udziwe kuti mtendere ulibe. Mayi Mary Chilima akulira ndikutitu kulira kupempha chithandizo Kwa akufuna kwabwino kuti afufuze za imfa ya mamuna wake komaso yemwe adagwetsa ndegeπŸ’”πŸ˜­πŸ˜­

Tiyeni yonse tigwirani mania kuti chilungamo chidziwike ndithu

Follow our page

28/09/2024

Pangani follow page yanga guys

28/09/2024

Game on bangwe 1 noma 0πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Asaaaa
20/09/2024

Asaaaa

18/09/2024

πŸ‘οΈ

Address

Blantyre

Opening Hours

Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zanthu zomwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category