Mzika Network

Mzika Network Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mzika Network, Africa-Malawi, Blantyre.
(1)

26/11/2025

Big shout out to my newest top fans! Msowoya Ntchindi Lillian, Prom Ice Mandala, Yakobe Kandulu, Namalele Bless, Zaithwa Mandanda, Chisomo Angelz Maluwa, Aysha Son Dota, Maggie Nafe Chilemba, Jasten H George, Lesten Ahmad Kumwanje, Hastings Phukaphuka Banda, Justin Mkwapatira, Carol Chikungwa, Theophilus Pekah, Fiona Nangantani, Janet Chikadzuma, Çarlœs Êrïc, Chunga Kakhoza Racheal, Angella Master, Rejoice Nina, Chauma Banda Esimie, Cid Tholi, Lucius Mw, Brian Banda, PhillIp Cosmas, Precios Njalah, Davis Pwele Singini, Davie Kamphungu, Aubrey Kachala, Clenter Dzombe, Praise Shaba, Ambiri Akutero, Patricia Nandaya

 Mmodzi mwa a luso losangalatsa anthu mmalawi muno kudzela mma comedy ake Mr Jefu wati ngakhale amachita ma comedy akewa...
05/04/2025



Mmodzi mwa a luso losangalatsa anthu mmalawi muno kudzela mma comedy ake Mr Jefu wati ngakhale amachita ma comedy akewa koma munthuyu sali bwino ai .Vuto lalikulu lomwe ali nalo mkuluyu ndi la mwendo.Mwendowu wakhala ukumuvuta nthawi yaitali kuthamangila zaka zinayi tsopano.Ngati bambo amayesetsabe kudzilimbitsa poti ali ndi banja lomwe limadalila iwowa .Ayeselapo kufikila anthu kuti awathandize koma izi siziphula kanthu poti palibe yemwe amachitapo kanthu pa vutoli.Ndalama yomwe ikufunika kuchipatala ndi yokwana 3.3million kwacha kuti mwendowu uchitidwe operation .Akupemphabe kwa omwe angakwanitse kuwathandiza poti ofuna thandizo satopa.Pofuna kuva zambiri mungalumikizane nawo pa 0994997723

Ambuye akudalitseni nonse,amene muthandize🤝

MMr Jefu tiseke comedy

05/04/2025

Happy Sabbath Day Mzika!🌅

Friday lanu likuyenda bwanj kumeneko?Kuno likuyenda bwino,monga pa chi batchala🤣
04/04/2025

Friday lanu likuyenda bwanj kumeneko?

Kuno likuyenda bwino,monga pa chi batchala🤣

04/04/2025

Ambuye akutetezere ndi kudalitsa moyo wako masiko onse Amen🙏

 Lingadzi House yabuka moto ku City Center mu mzinda wa Lilongwe omwe wayamba chifukwa cha Magetsi.
03/04/2025



Lingadzi House yabuka moto ku City Center mu mzinda wa Lilongwe omwe wayamba chifukwa cha Magetsi.

 Mphunzitsi wapa School ya Milonde, Mitundu zone, Lilongwe Rural East wapezeka atadzimangilira . Malemuwa asiya Will ya ...
03/04/2025



Mphunzitsi wapa School ya Milonde, Mitundu zone, Lilongwe Rural East wapezeka atadzimangilira . Malemuwa asiya Will ya momwe makobidi ake azagawidwire . Iwo anati ndalama zawo zikatuluka omwe anali nawo ngongole adzapatsidwe ndipo maina awo alembelatu pa kalatayo.

 Mfumu ya Mudzi mwa Maula m'dera la mfumu yaikulu Zulu.Amangilira pa mtengo atadya ndalama za adzukulu akumanda.....Adzu...
02/04/2025



Mfumu ya Mudzi mwa Maula m'dera la mfumu yaikulu Zulu.Amangilira pa mtengo atadya ndalama za adzukulu akumanda.....

Adzukulu akumanda ali ndi malamulo awowo kusiyana ndi amudzi,kotero kumangidya kwa mfumuyi agwilira ntchito malamulo awo.

Phunziro: Kukhala ndi udindo sichinthu choti tiphwanyire lamulo,palibe ali pamwamba pa lamulo.

01/04/2025

Mzika! talowa mwezi wa April, mwezi number four.Tsiku lisathe usanakunge Pemphero zikuyendere mwezi uno Amen🙏

01/04/2025

Mzika ife timakhulupira mulungu.

Choncho mulungu sanalenge chitsiru nde ife sitipanga nawo.

Address

Africa-Malawi
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mzika Network posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mzika Network:

Share