Tchado Mphatso M.K.Charlie

Directions

Tchado Mphatso M.K.Charlie Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tchado Mphatso M.K.Charlie, Grocers, Area 49 Newshire, Lilongwe.

Football
29/08/2025

Football

21/08/2024

Kampani ya maulendo a ndege ya Nyasa Express yatsimikiza kuti ndege yawo ya mtundu wa Cessna C210 yomwe nambala yake ndi 7Q-PFU yagwera m'nyanja ya Malawi ku Nkhotakota.

M'chikalata chimene asainira ndi mayi Bridget Sefu, kampaniyo, imene imakonza maulendo a ndege molingana ndi kufuna kwa makasitomala, ndegeyo inanyamuka pa bwalo la Tongole ku malo osungira nyama za ku thengo a Nkhotakota Wildlife Reserve kupita ku Liwonde National Park m'boma la Machinga.

"Ndegeyo munali okwera awiri ndi woyendetsa mmodzi. Mmodzi mwa okwerawo wapezeka ndipo amayenda yekha koma amutengera ku chipatala kuti akamuyeze zina ndi zina," atero a Sefu.

Iwo ati ndegeyo siyinapezeke ndipo ntchiyo yosaka ili mkati.

Ndege ya mtunduwu imanyamula anthu 6 ndipo imaoneka ngati ili m'chithunziyo.

Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu atsimikiza za nkhaniyi.

THE Cap nickless K7,500 onlyFind me 0984027653 wap
21/08/2024

THE Cap nickless K7,500 only
Find me 0984027653 wap

20/08/2024
20/08/2024

Mwakhalapo pali infa
Ngati amakutetezela

AMEN
Amakwana kwaiyeyo
πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™

Address

Area 49 Newshire
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tchado Mphatso M.K.Charlie posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category