Awiri Beverages

Awiri Beverages We manufacture very tasty freezes in the following flavours:

1. Cola
2. Creme Soda
3. Raspberry
4. Orange
5. Pineapple

Happy Mother's Day to all our customers ! Mwana mkazi thamanga basi, pakhomo pasasowe mchere.🔥🔥 Super Cool Freezes ndi d...
15/10/2025

Happy Mother's Day to all our customers ! Mwana mkazi thamanga basi, pakhomo pasasowe mchere.🔥🔥 Super Cool Freezes ndi dhilu 🔥

Happy Mother's Day to all our mothers.Kuno ku Super Cool Freezes and Purified Sachet Water timakunyadirani kwambiri. Mul...
15/10/2024

Happy Mother's Day to all our mothers.

Kuno ku Super Cool Freezes and Purified Sachet Water timakunyadirani kwambiri. Mulungu azikudalitsani nthawi zonse!!

Kunja ndiye kwatentha.....koma musade nkhawa!!Imwani Super Cool Freezes kuti mumve kayaziyazi!!Dziko lonse linavomereza ...
18/09/2024

Kunja ndiye kwatentha.....koma musade nkhawa!!Imwani Super Cool Freezes kuti mumve kayaziyazi!!

Dziko lonse linavomereza kale kuti freezes ndi m'modzi basi ndipo Super Cool!!

Super Cool! Ndiye freezes yo!!

We are in Zomba once again tomorrow the 16th August 2024.Thondwe, 3 miles, Zomba, Matawale, Chinamwali, City Boundary, S...
15/08/2024

We are in Zomba once again tomorrow the 16th August 2024.

Thondwe, 3 miles, Zomba, Matawale, Chinamwali, City Boundary, Songani, Malosa konzekani mawa tili konko!!

Tikati freezes ndi Super Cool!! Try it you will never regret!!

We are in Zomba today!! Get in touch if you need some freezes.Lero tili Ku Zomba. Tipezeni mudzaode nawo freezes wabwino...
09/08/2024

We are in Zomba today!! Get in touch if you need some freezes.

Lero tili Ku Zomba. Tipezeni mudzaode nawo freezes wabwino wokoma uyu!

0999417333 tilankhuleni

Chikwawa, Nsanje, Zomba, Salima, Mchinji, Kasungu, Mangochi !! Mukuti bwanji? Tiyeni tiyeni tithamange basi
07/08/2024

Chikwawa, Nsanje, Zomba, Salima, Mchinji, Kasungu, Mangochi !! Mukuti bwanji? Tiyeni tiyeni tithamange basi

Kunja ndiye kwacha. Tithamange basi!.Super Cool Freezes ndi dhilu
23/07/2024

Kunja ndiye kwacha. Tithamange basi!.
Super Cool Freezes ndi dhilu

Attention: We are looking for an experienced technician in Reverse Osmosis machine installationContact 0999417333
13/12/2023

Attention: We are looking for an experienced technician in Reverse Osmosis machine installation
Contact 0999417333

03/10/2023

Mzuzu Tafika! Kulindila kwamala. Gulani freezes wa super cool mwalubilo. Komani makwacha ya pompo pompo

Yes! The wait is over..... Hurry get your stock and start minting the cash pompo pompo!

Contact +265 880 06 03 07/+265 988 55 67 88

We manufacture very tasty freezes in the following flavours:

1. Cola
2. Creme Soda
3. Raspberry
4. Orange
5. Pineapple

We are excited to have you onboard! You win we all win!Trevor Tiyanjana Mapulanga, Trancy Singini Banda, Treaty M Nyalug...
27/09/2023

We are excited to have you onboard! You win we all win!

Trevor Tiyanjana Mapulanga, Trancy Singini Banda, Treaty M Nyalugwe, Christar Kingston Applewhite, Mhango Nyirenda Queen, Diana Kaponda, Holy Wa Eness, Nancy Vitumbiko Mkondiwa, Happy Same, Charity Blessings Joomer, Cortinas Wanyawuzembe Ngwira, Triza Phiri, Collida Luhanga, Mirriam Nyirongo Phiri, Mwayi Kambala, Chisomo Thulan Demister, Tracy Tasneem Ziyaya, Ketty Teesue Wakhutamoyo, Jessy Banda, Patricia Chinthungo, Patricia Bwanali, Costance Mirriam Bango, Nambewe Jere, Chigonjetso Gomanie, Bridget Mbewe, Mimi Nasah Golozera, Tapiwa Mguntha, Agnes Mwanjasi Mwangailo, Demister Wayawaya, Vera Mtombosola, Tiyamike Nkhoma, Dorothy Manda, Solomon Kensi, Mathews Khokhokho MW, Emily Polela, Wezzie Mtumbuka Phiri, Atlanta Mtunda Ingainga

Kunja kwacha!  Kunja kwatentha!  Pezani phindu lochuluka, odani Super Cool Freezes lero. Pakhomo pasasowe sopo abale! Ti...
05/09/2023

Kunja kwacha! Kunja kwatentha! Pezani phindu lochuluka, odani Super Cool Freezes lero. Pakhomo pasasowe sopo abale!

Tipezeni lero pakapenga ku Limbe kapena ku Lilongwe pafupi ndi pep store imene ili kuseli kwa Sana yapa Mzikiti.

25/08/2023

Kunja kwacha! Kunja kwatentha! Pezani phindu lochuluka, odani Super Cool Freezes lero. Pakhomo pasasowe sopo abale!

Tipezeni lero pakapenga ku Limbe kapena ku Lilongwe pafupi ndi pep store imene ili kuseli kwa Sana yapa Mzikiti.

We manufacture very tasty freezes in the following flavours:

1. Cola
2. Creme Soda
3. Raspberry
4. Orange
5. Pineapple

Address

Kamuzu Procession Road
Lilongwe
207201

Opening Hours

07:00 - 17:00

Telephone

+265999417333

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Awiri Beverages posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Awiri Beverages:

Share