Ekali Farms

Ekali Farms OUR PRODUCTS: Maize, Onions, Pine Trees, Bananas and Avocados. FRUITS SEEDLINGS: Mangoes, Oranges, Lemons, and Pawpaw.

02/09/2026

Shout out to our newest followers! Excited to have you onboard! Phyllis H. Lyson, Miyaka Chapola Saidi, Kajamuh Farm, Kondwani Kampenya

Ekali Farms Ulimi wa Mbatata wayenda bwino chaka chino.Inshallah (God willing), we will do much better next growing seas...
30/08/2026

Ekali Farms Ulimi wa Mbatata wayenda bwino chaka chino.

Inshallah (God willing), we will do much better next growing season chifukwa taphunzira zambiri m'chaka chimenechi.

Ekali Farms Feeling satisfactory! 😇Ina mwa mbatata ya Nkholowa yomwe takolora.
29/08/2026

Ekali Farms Feeling satisfactory! 😇

Ina mwa mbatata ya Nkholowa yomwe takolora.

03/06/2026

Shout out to our newest followers! Excited to have you onboard! Dawdi Chimpeni, Austin Mwandoloma, Dan Chris Kalanguluka

23/05/2026

Shout out to our newest followers! Excited to have you onboard! Vanniex Huesen Smokoh, Yesaya Nthiwatiwa, Chikondi Mponda

Mbewu ya Zitheba (mtundu wa Blantyre). Tangotsala ndi 10KGs pa mtengo wa 20,000 MK pa KG. Location: LilongweCall/WhatsAp...
18/05/2026

Mbewu ya Zitheba (mtundu wa Blantyre). Tangotsala ndi 10KGs pa mtengo wa 20,000 MK pa KG.

Location: Lilongwe
Call/WhatsApp: 0881 07 77 40

Ekali Farms Mbewu ya Zitheba (mtundu wa Blantyre). Tangotsala ndi 10KGs pa mtengo wa 20, 000 MK pa KG. Location: Lilongw...
18/05/2026

Ekali Farms

Mbewu ya Zitheba (mtundu wa Blantyre). Tangotsala ndi 10KGs pa mtengo wa 20, 000 MK pa KG.

Location: Lilongwe
Call/WhatsApp: 0881 07 77 40

Ekali Farms  Tikugulitsa mbewu ya Zitheba (Green Beans) ya mtundu wa Blantyre.Mbewuyi ndi ya quality komanso ya chaka ch...
13/05/2026

Ekali Farms Tikugulitsa mbewu ya Zitheba (Green Beans) ya mtundu wa Blantyre.

Mbewuyi ndi ya quality komanso ya chaka chino.

Location: Lumbadzi, Dowa Turnoff

Call/WhatsApp: 0881 077 740

Ekali Farms  Tikugulitsa mbewu ya Zitheba (Green Beans) ya mtundu wa Blantyre.Mbewuyi ndi ya quality komanso ya chaka ch...
11/05/2026

Ekali Farms Tikugulitsa mbewu ya Zitheba (Green Beans) ya mtundu wa Blantyre.

Mbewuyi ndi ya quality komanso ya chaka chino.

Mtengo: MK 25, 000 per KG
Location: Lumbadzi (koma timatumiza at your cost)

Call/WhatsApp: 0881 07 77 40

Address

Lumbadzi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ekali Farms posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category