Kalibu-Lek Cafe & Restaurant

Kalibu-Lek Cafe & Restaurant Kalibu-Lek | Mangochi, Malawi. Food that beats your cravings. Serving locals & global travelers

Snacks. Meals. Birthdays. Cocktails. Family dining. Good vibes.

Coffee

Great food. Health boost drinks. Excellent service

Mtakataka Turn-Off, Mangochi.

Kumadya bwinotu.Lero tikugawa zakudya kwinaku tikusangalala koposa. Mmodzi waife ku Kalibu-Lek kuno anabadwa lero.Ameney...
17/08/2026

Kumadya bwinotu.

Lero tikugawa zakudya kwinaku tikusangalala koposa. Mmodzi waife ku Kalibu-Lek kuno anabadwa lero.

Ameneyu ndi Shyrex. Happiness ili 🔥🔥

Kumadya bwinotu eti!Mwawadziwa wamkulu Skeffa?
16/08/2026

Kumadya bwinotu eti!

Mwawadziwa wamkulu Skeffa?

Kumadya bwinotu paja. Pa chi Sunday. Ndipo okupatsirani zabwinozo ndi ifeyo.Kudya zokoma kwambiri kunyanja kuno sikobowo...
16/08/2026

Kumadya bwinotu paja. Pa chi Sunday.

Ndipo okupatsirani zabwinozo ndi ifeyo.

Kudya zokoma kwambiri kunyanja kuno sikobowola nthumba.
Kudya zokoma kunyanja kuno nkopezekeratu ndi Kalibu-Lek.

Osaphweketsatu. Ngati simunafike apapa, inuyo kunyanja simunafikeko.

The Port. Potelera ndi Ponyamukira

Kumadya bwinotu. Pizza uyuyu palibenso! Ife timadyetsa bwino koposa. Kaya mugula nokha kaya mupeza bayala, mission - Iti...
15/08/2026

Kumadya bwinotu. Pizza uyuyu palibenso!

Ife timadyetsa bwino koposa.

Kaya mugula nokha kaya mupeza bayala, mission - Iti welo (Eat well).

Good food, good vibes. BEAUTIFUL memories

Kumadya bwinotu.Ife timadyetsa bwino koposa. Kaya mugula nokha kaya mupeza bayala, mission - Iti welo (Eat well).Good fo...
15/08/2026

Kumadya bwinotu.

Ife timadyetsa bwino koposa.

Kaya mugula nokha kaya mupeza bayala, mission - Iti welo (Eat well).

Good food, good vibes. BEAUTIFUL memories

Employment opportunityKalibu-lek Cafe & Restaurant - Monkeybay. Waitress x 1 PositionWaitress Intern x 1 PositionThe des...
10/08/2026

Employment opportunity

Kalibu-lek Cafe & Restaurant - Monkeybay.

Waitress x 1 Position
Waitress Intern x 1 Position

The desirable candidate will demonstrate capacity to serve guests in outstanding manner, as well as attention to detail with a service value of - every guest is royal.

The eatery hosts guests from all walks of life. Hence, ability to communicate in English will be an added advantage.

Please send the required documentation via WhatsApp to 0995665978 or email [email protected].

Closing date - 17 August 2026.

https://emaps.app.goo.gl/KGtFHPRfM5U6p6CRA

Mwayi WantchitoKalibu-lek Cafe & Restaurant - Monkeybay. Waitress x 1 PositionWaitress Intern x 1 PositionTikufuna anthu...
10/08/2026

Mwayi Wantchito

Kalibu-lek Cafe & Restaurant - Monkeybay.

Waitress x 1 Position
Waitress Intern x 1 Position

Tikufuna anthu odziwa kuseva mwachifumu, mwaukadaulo ndi mwachidwi.

Pamalopa pamafika anthu ochokera madera osiyanasiyana. Kudziwa kuyankhula chizungu pang'ono, kuwonjezera mwayi wanu.

Tumizani zokuyenerezani ku 0995665978.

Tsiku lotseka - 17 August 2026.

https://emaps.app.goo.gl/KGtFHPRfM5U6p6CRA

Odziwa kudya life, amadyera mmbali mwanyanja.Osati kumapiri or ntchire ngati anthu okhwima. Akufuna kungodya kathanzi.Os...
06/08/2026

Odziwa kudya life, amadyera mmbali mwanyanja.
Osati kumapiri or ntchire ngati anthu okhwima.

Akufuna kungodya kathanzi.

Osati maspice mbwee. Ataa!

Yakwana yokha nthawi ya nkhomaliro.Whatever is happening in your life, eat well. Make sure you lek it in style. Eat to e...
06/08/2026

Yakwana yokha nthawi ya nkhomaliro.

Whatever is happening in your life, eat well. Make sure you lek it in style.

Eat to enjoy not to survive or commit su***de. Kalibu-Lek makes it happen for you

Ngati muli pa changu zedi, bukani / odani in munthawi yabwino - 0995665978.

Get a snack. Some drink. Smiles all the way. We beat your cravings.
29/07/2026

Get a snack.

Some drink.

Smiles all the way. We beat your cravings.

Address

Kalibu-Lek Cafe And RestaurantM10, Malawi+265 995 66 59 78https://maps. App. Goo. Gl/7N57ZCYYv4pFKrX 16
Mangochi
00265

Opening Hours

Monday 06:00 - 22:30
Tuesday 06:30 - 23:00
Wednesday 06:30 - 22:00
Thursday 06:30 - 23:00
Friday 06:00 - 23:59
Saturday 05:00 - 23:55
Sunday 06:00 - 23:45

Telephone

+265995665978

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kalibu-Lek Cafe & Restaurant posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kalibu-Lek Cafe & Restaurant:

Shortcuts

Share