AFCOP Poultry MW

AFCOP Poultry   MW The leading trusted supplier of Pure breeds of Poultry. Currently we are Supplying Sasso , Kuroiler and Black Australorp (Mikolongwe) breeds.

We are located in Ntcheu at Boma behind Agora store. You can also contact us via our number +265981685672

Timalizitse mafumukazi athu motere kwalero, and aja tinali ndi atatu. Abwenzi meet Hellen Wa A Lapani . M'modzi mwa alim...
22/05/2026

Timalizitse mafumukazi athu motere kwalero, and aja tinali ndi atatu. Abwenzi meet Hellen Wa A Lapani . M'modzi mwa alimi opezeka ndikutsatira maphunziro athu nthawi zonse.

10 points bonus.

Next! Tiwone Mafumu atatu tsopano. Mwinatu ndi inu😊, tikufuna kuwonako new names abwenzi tazionekani kkkkk

" MLIMI WOTSOGORA AMAWERENGA "

Eliza Jada Mdala , Another Queen for today. Abwenzi mumatilimbikitsa pakupedzeka kwanu komanso chidwi pamaphunziro athu ...
21/05/2026

Eliza Jada Mdala , Another Queen for today. Abwenzi mumatilimbikitsa pakupedzeka kwanu komanso chidwi pamaphunziro athu pano pa AFCOP Poultry MW nthawi zonse. 10 points bonus.

Ma Comment olimbikitsa umodzi ndi mtendere nthawi zonse.. pitirizani kukhala bwino ndi anthu. Pamenepa ndiye kuti ma points anu akwera kufika pa 29 (previously 19).

" MLIMI WOTSOGORA AMAWERENGA ! "

OUR FIRST QUEEN TODAY ! Meet Na Cha  Abwenzi! Theme : " LOTO LISAFE "10 points bonus to you. Kubweretsa ma points anu pa...
21/05/2026

OUR FIRST QUEEN TODAY ! Meet Na Cha Abwenzi!
Theme : " LOTO LISAFE "

10 points bonus to you. Kubweretsa ma points anu pa 34 (24 +10 ) mosawerengetsera current rewards. 2 more ladies remaining abwenzi.

" MLIMI WOTSOGORA AMAWERENGA ! "

NOW IS THE TIME! Posachedwapa maphunziro athu ayambenso. Abwenzi, mwakomzeka? Pamene tikusangalala kufika 10K, tipereke ...
21/05/2026

NOW IS THE TIME!

Posachedwapa maphunziro athu ayambenso. Abwenzi, mwakomzeka?

Pamene tikusangalala kufika 10K, tipereke sawatcha wa ulemu kwa abwenzi atatu (ladies first) pokhazikika (consistency ) pa zochitika zawo pa AFCOP Poultry MW . 10 points aliyense.

Ati nanga mphongo mwazisiya kuti... Zonse ndizotheka mu nthawi yake Abwenzi.

MALONDA
1 week old and 5 weeks old zilipo lero, kupangira aja amati mundisungire mzatenge pa 2, Nkhuku sitisunga pa msinkhu umodzimodzi ngati sopo chifukwa zimakhala zikukura tsiku ndi tsiku.

AFCOP Poultry MW
" Your Trusted Poultry Partner"

0981 68 56 72
NTCHEU BOMA (MPHATE)

 fans Ochepa okha ndi amene akutumiza activity yawo, posachedwapa tikamalengeza ma points ambiri akhala odabwa mkumafuns...
18/05/2026

fans Ochepa okha ndi amene akutumiza activity yawo, posachedwapa tikamalengeza ma points ambiri akhala odabwa mkumafunsa kuti nanga ine bwanji?

Werengani modekha ndikumvetsetsa dongotsolo la AFCOP POULTRY REWARDS potobwanya link ili ku comment box, yi.

OFUNA KUGURA NKHUKU
Lero ma 5 weeks alipo komanso kwa iwo ofuna kusungitsa ma 1 week apezeka lachisano lomweli.Onani mitengo mzithunzimu komanso tiyimbireni phone kuti tikuthandizeni mwachangu.

AFCOP Poultry MW
0981 68 56 72

NTCHEU BOMA (MPHATE)

Thanks Mose Chisoni , ALIPO FARM NDINU MADOLO ! Maphunziro ochita kusamba posachedwapa.... 10K wanunkhira kale uyu.  Ena...
16/05/2026

Thanks Mose Chisoni , ALIPO FARM NDINU MADOLO !

Maphunziro ochita kusamba posachedwapa.... 10K wanunkhira kale uyu. Ena akuti ' ife sitikudziwa chilichonse chokhudza kawetedwe ka Nkhuku....' . Mwafika malo oyenera inuyo osadandaula!

MUKAPEZA MBEU YENIYENI YA MTUNDU WA SASSO KOMANSO KUROILER SIMUDZAKHUMUDWA; 👉Kupilira kumatenda👉Kutha kusamalidwa ndi th...
15/05/2026

MUKAPEZA MBEU YENIYENI YA MTUNDU WA SASSO KOMANSO KUROILER SIMUDZAKHUMUDWA;

👉Kupilira kumatenda
👉Kutha kusamalidwa ndi thandizo lomwe lilipo panthawiyo (adaptability)
👉Kukura bwino
👉Madzira aakulu komanso okoma kwambiri
👉Ndi zina zambiri....

" Ubwino wa Nkhuku izi umapitilira mzelu za alimi ambiri, kuyitenga bwino mitundu imeneyi umphawi uja watha basi ". AFCOP Poultry MW ili pano kutsegura mzelu zatsopano mu ulimi wa Nkhuku.

TAWAUZENI AWO KUTI ASACHEDWE KUTIYIMBIRA PHONE KUTI APEZE MBEU YAWO. MITENGO YATHU ILI MZITHUNZIMU.

AFCOP Poultry MW
0981 68 56 72

NTCHEU BOMA

MA TOP FAN !  OSAKHALIRA BADGE. AFCOP POULTRY REWARDS, ZIKUTHEKA! Meet Akula Kampira  .MLIMI WOKHALA KU NTCHEU
14/05/2026

MA TOP FAN ! OSAKHALIRA BADGE. AFCOP POULTRY REWARDS, ZIKUTHEKA!

Meet Akula Kampira .
MLIMI WOKHALA KU NTCHEU

 fans . OSAKHALIRA BADGE!
13/05/2026

fans . OSAKHALIRA BADGE!

GOOD MORNING ABWENZI! Pamene ena akuzawombora anapiye awo ena amene tikufuna kugura ma day old mwayi wathu ndi womwewuns...
13/05/2026

GOOD MORNING ABWENZI!

Pamene ena akuzawombora anapiye awo ena amene tikufuna kugura ma day old mwayi wathu ndi womwewunso.

Nkhuku za Mtundu wa Sasso komanso Kuroiler ndi Nkhuku zomwe zikasamalidwa bwino zimakhala yankho lokhazikika pa ulimi wanu wa Nkhuku. Osaweta Mwachidzolowezi, dziwani mitundu yopinduritsa.

AFCOP Poultry MW : " Your Trusted Poultry Partner "

NTCHEU BOMA
0981 68 56 72

12/05/2026

fans ALIPO WAKOMZEKA KUWOMBORA ANAPIYE MAWA?

GOOD AFTERNOON ALL.

Address

Ntcheu Boma
Ntcheu

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Sunday 08:00 - 17:00

Telephone

+265981685672

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when AFCOP Poultry MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to AFCOP Poultry MW:

Share