Mkanga

Mkanga Tinasankha kupanga ulimu waziweto komanso mbewu. Aliyese atha kukhala mulimi🐐🚜🌱🐷πŸ₯­

Khumbo lathu ndikuphunzira zambiri za ulimi komanso kuphunzitsa ndi kulimbikitsa ena, maka achinyamata, kuyamba ulimi.

26/04/2026

THE BREED I GOOD FEED I GOOD CARE

Not for sale at the moment

17/04/2026

Them: Hello Mkanga, how do you manage to have 600+ 🐐🐐 🐐 at the farm?

Me: By adding one goat at a time

Ulendo makosana, umafupika mukamayenda. Yambani.

16/04/2026

April ndiye tikukankha

"The goat we bought from you has today given us ka mixed boar stud πŸ™" akutelo anzanu amene anayamba. Ambiri amapeza zama...
15/04/2026

"The goat we bought from you has today given us ka mixed boar stud πŸ™" akutelo anzanu amene anayamba. Ambiri amapeza zamawere kale kuno.

13/04/2026

Lero kuli busy kuno.
Izi zaswa chidzulo-dzulo.

Kuweta, musamati iyayi ine ndikufuna zamapasa aaaagh iyayi. Tawetani mbuzi zamisinkhu yabwino komanso zotha kulera ana basi.

Awuzeni a bae kuti dhilu ndi iyiyi kwinaku AI is taking over.

13/04/2026

Lerotu ku Mkanga

Kwa amene tinayamba, tiyeni osafooka.
Kwa amene sitinayambe, now is the best time.
Kwa amene sitiyamba, tiyeni tiwafunire zabwino amene akuyamba.

13/04/2026

Last year we tried beans and onion. Both did great, very good. We have however chosen to proceed with anyezi. Mbewu tinafesa and pano tayamba kuwokera. Mbewu ina ikadali yaying'ono pa nazare and nazare ina tikhala tikufesa ma sabata akubwerawa.

Mvula inagundikayi inatiwonongera nazare koma sitinagonje and we will keep pushing.

I will explain why we have gone onion way and not beans. A lot of factors were looked into.

Mwadzuka anzanga,Don't be afraid to start. You could be the game changer. People,  I mean a lot of people could build th...
12/04/2026

Mwadzuka anzanga,

Don't be afraid to start. You could be the game changer. People, I mean a lot of people could build their dreams off your shoulders, your success.

Look around, more often than not, a radio station or newspaper is not owned by a person who studied media, many academic agriculture experts do not own a poultry farm or just a vegetable garden and masters of accounting, you call them accountants, ambiri ndalama alibe, amangowerenga zawena.

Ulimi uwuwu umangofunika chidwi amangwetu, sukulu ya asamunda isakupangitseni kuwuona ulimi ngati wamakape. Muli phindu umumu.

It is until you embark on a bold agric expedition that someday you will employ those accountants to do financial reports and projections for you, agriculture experts will help you increase production and productivity and the journalists will do PR and communication for you.

Koma, zikufunika muyambe. Ndipo yambani ndizimene mulinazo.

Mwadzuka bwanji ma guy?Yambani ndi zimne muli nazo lero. Muyambire pamene mulipo.
11/04/2026

Mwadzuka bwanji ma guy?

Yambani ndi zimne muli nazo lero. Muyambire pamene mulipo.

10/04/2026

Meanwhile we have been adding one goat at a time. Osadikira zamapasa mukafuna kuyamba kuweta. Tawuyambeni ulendowu zabwino muziona nkati mwandime.

Here is what you need to know, you will never get the time back. Never ever. If you have to start, do so now.

10/04/2026

These are One Month and Ten Days old today. We are right on track with these ones unlike the first group. .

Remember, make plans before that money comes. When it arrives and finds none, it will make a trillion plans for you and mupezeka mwagula iPhone17

09/04/2026

Two Months, Nine Days (We are slightly behind, we will catch up)

Don't always wait for the perfect time, time is an excellent perfecter

Address

Salima

Telephone

+265999826757

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mkanga posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mkanga:

Share

Category