Life with Tiya

Life with Tiya Let's grow together ❤️

20/04/2026

Kodi munthu akakuuzani kuti I love you mumayankha kuti chani ine ndimayankha kuti Amen 🤭 ndikulakwisa?

Congratulations to us.... Sealed
18/04/2026

Congratulations to us.... Sealed

13/04/2026

Kuti tionesese ambiri omwe akumati sangakwatile mkazi WA mwana kale ndi anthu Oti anasiya ana penapake samawathandizaso
Ena ndi amuna amabanja omwe akulela ana Oti si awo Iwo akuona ngat ndi awo osadziwa anayendedwa Njomba 🤣🤣🤣
Apa tingoti ambiri makomomu tikulela ana Oti si athu koma sitikudziwa🤣🤣🤣

10/04/2026

Kwa amuna omwe anakwatila mkazi WA mwana kale tabwerani tinvane chinthu chinachake chanzeru.

Ndaona post inayake imene ikunena kuti olo mukathandiza mwana ompezayo chanu palibe malamulo samakuonani inu ngati kanthu komano 1 thing you should know is that mwana Oti wamulela wekha mwachikondi samakuiwala moyo wake onse ndipo amakuonani inu ngati hero, kuthandiza mwana WA munthu wina sizitathauza kuti ukufuna mwanayo akhale wako kapena uzadyepo ichi ndi chikondi chomwe muli nacho pa mayi wa mwana chomwe chikupitaso Kwa mwana.

Ndiye anthu osowa chikondi ndi osowa malangizo asakubwezeni pambuyo do whatever it takes to take care of that child educate that child and don't think of anything negative.

Mwana ompeza naye ndi munthu amafuna chikondi chisamalilo.

04/04/2026

Koma tchipisi chilipoo?🥺🤔

Eya ndine virgin koma ndili ndi mwana modzi🤣🤣 otsutsayo zake
31/03/2026

Eya ndine virgin koma ndili ndi mwana modzi🤣🤣 otsutsayo zake

Inu maganizo Anu ndi otani a nkhan yosafuna kukwatila nkazi WA mwana kaleyi🤭🤭🤭🙌
29/03/2026

Inu maganizo Anu ndi otani a nkhan yosafuna kukwatila nkazi WA mwana kaleyi🤭🤭🤭🙌

28/03/2026

Munthu ndamuuza I love you akuyankha kuti ineso aaaah za ziii ineso chani 🤣🤣

27/03/2026

Nchifukwa Chan azibambo ambiri Amati mkazi WA mwana kale iwowo ayi?
Azibambo tiuzeni zifukwa zanu

27/03/2026

Bola kukwatila mkazi WA mwana kale kusiyana ndi Ochosa mimba
Ndanena ndanena🤣🤭

Address

Sadzi
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Life with Tiya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share