Atizey mz

Atizey mz Atizy mz

08/12/2025

____/"""!.....
[=@===@==] PiPiiii.Estou na recolha de pessoas especiais para 2026.O preÇo da viagem é saude,amor,paz e um prospero ano novo, espero que vamos juntos para (2026). Nao priva essa sms envie as pessoas especias da sua vida,se eu for uma deles devolve-me.

08/12/2025

Boyfriend mpaka kumupempha ya fertilizer,🤔🤔😂😂😂,polani moto atsikana.

Pena que minha amiga, não apanhou nada.

08/12/2025

Celta endireitou Real Madrid 😭

19/11/2025

Anthu anapita kukaona ng'ona Koma ali pakati pa dam, mwini malowo anati, yemwe angagwere mu dam ndipo mkukatulukira tsidya linalo amupatsa 10 million dollar.

kunali ziiii kwa 5 minutes koma posakhalitsa anangoona mkulu wina wagwera ndipo ng'ona zinayamba kumuthamangitsa koma sizinamugwira mpaka anakatulukira tsidya Lina, pompo pompo mwini dam uja anatenga ndalama ija ndikumupatsa ...

Mkulu uja ali ku room ndi mkazi wake anayamba kumuuza kuti "umadziwa mu dam muja sizoti mnachita kugweramo ndekha koma munthu anachita kundikankhiramo" Mkazi wake uja anamwetulira kwinaku akuti mnakukankhira ndinetu..

Mwaphunzirapo chani pa nkhani imeneyi?

19/11/2025

Mudzakafa⚰⚰💔😭

Anthu akumudzi kwanu azakhala pansi kulemba program ya maliro anu, azatuma azimayi omwe umati ndi Afiti, osasamba, onukha thukuta aja asokhe ufa, ndipo ena azasokha ngakhale alibe oti adye madzulo💔⚰
Anyamata amudzi omwe mumati nda mowa komaso achamba aja asakumba manda anu😭😭⚰ chonsecho olo 50kwacha sunawagailepo koma sakhumudwa.
Ana onse week imeneyo sazapita ku school azatumiza uthenga kuti mudzi mwao mwachitika maliro💔😭 chonsecho olo copy sunawagulireko.
Azibambo azatha week osapezeka pa bawo, akuti kupeleka ulemu kwa mtembo wako😭😭😭⚰⚰💔💔

MA FRIENDS A TOWN.

Azafika kumudzi kwanu atagula zakudya zao akuti sangadye zophika anthu amudzi zosalongosoka, azamwa madzi a botolo ogula akuti sangamwe akumudzi atha kudwala mmimba, ndipo.azamuza oyendesa program kuti apange changu achoka kutali ndipo nseu wanu ndiovuta kuyenda ndi galimoto, azajambulitsa pa nthumbila yako💔💔 azapanga post pa fb komaso azaika status pa wap, azalemba R l P bro/sister, azanyamuka maliro ako asanamalize kukwilira manda😭😭😭 ndipo azakaima pa Liquor shop town ndikumamwa mowa🥃 kuiwala zaiwe😭😭😭💔💔⚰⚰⚰⚰ CHIKONDI CHA MA FRIEND APADZIKO.

GUYZ Chikondi cheni cheni chili kwa anthu akumudzi ndipo sakwiya ngakhale tisamawathandize, tikapita amatiphikila nsima ya ufa oyera bwino mwina makomo 7 kubwelesa nsima akuti udya, chonsecho sunawagulire or Bonya💔😭😭😭

Mulungu akakudalitsani muziwakumbukako abale ndi anasi Kumudzi😭😭😭😭😭⚰⚰⚰

Ambuye akuthangatileni utsiku uno🙏🙏

15/11/2025
12/11/2025

EU posso ser b***o em inglês mais pelo menos sei que beautiful significa bateria full😹😹😹

12/11/2025

Nde kuli amuna ena
Iwowo mowa ayi
Kusuta ayi
Nkhanza ayi
Mpira ayi
Kuba ayi
Iwowo koma chani kodi?………

12/11/2025

CHIDWI NDI NTHAWI YOMWE MUMAYIKA MU MPIRA ⚽️
MUNAKAKHALA KUTI MUMAYIKA MU MOYO WANU BWENZI MULI PATALI KWAMBILI. MUNTHU ULI M’MALUZI KOMA ULI BIZE NDIZA MPILA KUNYUMBA KULIBE NDIWO.

12/11/2025

Za anthu omwe anali mma gang (magulu a upandu) ku Elsavador, amene ali ku CECOT prison.

Ndinaiwala kunena kuti, pamakhala test kuti alowe mmaguluwo.

Test yoyamba ndiyakuti aphe m'bale wawo kapena kholo lawo. Akakwanitsa, nde amalowa nawo mu gang.

Nkona El Salvador inkatchedwa 'murder capital' ya dziko lapansi dzaka za m'mbuyomu.

Endereço

Tete

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Atizey mz publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Atalhos

Compartilhar

Categoria