22/08/2026
π CHILUNGAMO ONLINE β TOGETHER WE CAN! π€
Panopa ife ngati Chilungamo Team timakhala osangalala kwambiri kuona kuti pa zomwe timalonjeza kuti tiphunzitsa, timayesetsa kuzikwaniritsa ndithu. π
Ngakhale tili ndi zinthu zochepa zomwe tili nazo, timayesetsa kuphunzitsa aliyense amene ali ndi chidwi chophunzira, osatengera kuti ndinu ndani kapena mumachokera kuti.
π― Cholinga chathu chachikulu ndi kuthandiza anthu, makamaka omwe akufuna kuphunzira luso latsopano kuti ayambepo kutakataka ndi kupanga ndalama.
Ngakhale pali anthu ena omwe safunira anzawo zabwino ndipo amakhala akuti opseza kuti tisiye kuphunzitsa, ife sitingalole zimenezi kutilepheretsa. Tidzapitiriza kuphunzitsa, kulimbikitsa komanso kuthandiza anthu momwe tingathere. β€οΈ
Dzulo tinaphunzitsa SAUSAGE MAKING π ndi SWAN FREEZERS π¦, ndipo ophunzira athu anakondwera kwambiri ndi zomwe anaphunzira. Tikukhulupirira kuti ambiri ayamba kugwiritsa ntchito luso limeneli kuti ayambepo kuchita zinthu zawo.
Pa SOAP MAKING π§Ό, ambiri omwe tinawaphunzitsa kale ayamba kupanga. Izi zimatipatsa mphamvu kwambiri chifukwa timafuna kuona kuti knowledge yomwe timapereka ikusintha kukhala action. πͺπ₯
Tikudziwa kuti tonse sitingathe kupezeka pa training iliyonse chifukwa ma priorities athu amasiyanasiyana. Ena amakhala busy, ena amakhala ndi zinthu zina zofunika kuchita.
Koma ngakhale zili choncho, KNOWLEDGE NDI YOFUNIKA KWAMBIRI. π
Luso lomwe mungaphunzire lero limakhala chiyambi cha kusintha kwa moyo wanu patsogolo. Musadikire mpaka zinthu zonse zitakhala bwino kuti muyambe. Yambani ndi zomwe muli nazo, phunzirani zomwe mungathe, ndipo pitani pang'onopang'ono. π
π₯ NEXT TRAINING β SEPTEMBER π₯
Tikukonzekera SOAP MAKING TRAINING, ndipo mtengo wake udzakhala wotsika kwambiri, monga momwe timachitira nthawi zonse kuti anthu ambiri athe kutenga nawo mbali.
π€ NANGA INU MUNGAKONDE MUTAPHUNZIRA CHANI?
π§Ό Soap Making
π Sausage Making
π¦ Freezers Making
π Baking
ULIMI WA bowa
ππ Tiuzeni mu COMMENTS!
Tikufuna kumva kuchokera kwa inu kuti tidziwe zomwe ambiri mukufuna kuphunzira komanso zomwe tingakonzekere mtsogolo.
To register for September training
WhatsApp us now 0986 79 52 67 or Dinan button la whatssaplo mutipeza mwachangu
Kwa omwe so mukufuna ku order swan freezers alipo ndithu pantengo waziii tiyakhurei
β€οΈ TOGETHER WE CAN