Grace 2 sadzu

Grace 2 sadzu you are welcome to my page, feel free to ask and read ๐Ÿ“š my stories
(4)

Ntchimo limazuzatu .Wina wakomokaso , kodi angakhale ndani.Part 11 ifika ndithu osatopa kudikila .
27/09/2026

Ntchimo limazuzatu .

Wina wakomokaso , kodi angakhale ndani.

Part 11 ifika ndithu osatopa kudikila .

Kwatichela tsopano. Chantel ndi frank. Mulipo eti ?
27/09/2026

Kwatichela tsopano.

Chantel ndi frank.

Mulipo eti ?

Nkazi wanga ankakonda kuvula ring yomwe tinamangila ukwati ikafika nthawi yausiku okha okha ndipo sindinadziwe kuti..Kod...
27/09/2026

Nkazi wanga ankakonda kuvula ring yomwe tinamangila ukwati ikafika nthawi yausiku okha okha ndipo sindinadziwe kuti..

Kod tilipo omwe tawelenga kankhani apa Mu episode 1?

Usiku wabwino,  Mugone bwino nose,  tionaneso mawa
26/09/2026

Usiku wabwino,

Mugone bwino nose, tionaneso mawa

Kodi mukuona ngati bambo okana mwanayi akupepesa chani ?Kodi mawa tikhale pa holiday kapena ayi.
26/09/2026

Kodi mukuona ngati bambo okana mwanayi akupepesa chani ?

Kodi mawa tikhale pa holiday kapena ayi.

26/09/2026
Mwaswera bwanji. Apa ndikhulupilira tonse yaonela part 10.Ngat sinakupezeni link ndiika mu comment. Kodi ndindan ndindan...
26/09/2026

Mwaswera bwanji.

Apa ndikhulupilira tonse yaonela part 10.

Ngat sinakupezeni link ndiika mu comment.

Kodi ndindan ndindan apa nanga chimachitika ndichani?

Nkazi wanga ankakonda kuvula ring yomwe tinamangila ukwati ikafika nthawi yausiku okha okha ndipo sindinadziwe kuti ...E...
26/09/2026

Nkazi wanga ankakonda kuvula ring yomwe tinamangila ukwati ikafika nthawi yausiku okha okha ndipo sindinadziwe kuti ...

Episode 1..

Zinayamba tsiku loyamba lomwe tinamangitsa ukwati wathu .
Tsiku limeneli tili nkati mocheza, nkazi wanga adavula ring ndipo panthawi imeneyi sindinazindikile chilichonse.

Nkazi wanga anandiyang'ana ndipo anamwetulira , kenako anangoti .
Ndi nthawi yoti togone mamuna wanga.

Usiki wabwino nkazi wanga ,
Ndinangovomela koma sindinaganizilepo kanthu.
Ndinkaganiza kuti mwina watopa kwambiiri ndikuvuna paukwati.
Ndinagona pa bed nayamba kusekelera komaso kusangalala kuti ndakwatila.

Moyo unkayenda bwino koma sindinadziwe kuti kukubwela nkhondo kutsogolo kwanga.

Pang'ono ndi pang'ono ndinayamba kuganiza kuti chinachake sichilibwino.
Usiku ulionse nkazi wanga ankapita ku bed ring ili pachala.
Koma pakati pausiku ring ija ankayivula koma ma mm'awa kukacha , ring inkapezeka ili pachala chake.

Ulendo oyamba ndinalibe nazo chidwi.
Ulendo wachiwiri ndinazilimbitsa mtima ndipo Ulendo wachitatu ndinadziwa ndithu kuti pali kanthu.

Nthawi zambiri pakati pa usiku, ndinkamva akunenelera dzina langa ngati kuti akulankhulana ndi munthu.
Nthawi zina ankapita ku toilet ndipo sindinkamvetsetsa chomwe chikuchitika.

Tsiku lina kutacha , ndinaganiza zoti ndimufunse.

Kodi honey,
Usiku ulionse ukumavula ring ndipo kukacha ring ikumapezela pachala chako .
Kodi ndichifukwa chani?

Nkazi wanga sadayankhe zodziwika , adangobwela pafupi nkundipatsa hagi kenako anangolankhula mawu oti

Ndimakukonda James.

Madzulo kutada , ndinaganiza kuti ndisagone tulo kuti ndidziwe chifukwa chomwe nkazi wanga ankapangila izi .

Koma pakati pa usiku pasanafike , nkazi wanga adafunsa .

Kodi ndichifukwa chani iweyo.sukugona tulo ?

Basi kungoti ndimaseweletsa phone.
Ndinayamkha chomcho.

Panthawi yomweyi, nkazi wanga anayamba kukamba nkhani zosangalatsa komaso zopatsa chidwi .
Mpaka ndinagona tulo lofelatu

Ma mm'awa kutacha nthawi ili 8:00 am , adandigwila paphewa kundidzutsa.

Ndinali odabwa kwambiiri chifukwa sindinakumbukile momwe ndinagonela usiku wathawo .

Usiku otsatilawu ndinayeselaso kukhala mmaso koma zinakanika .
Ndinangozindikila kuti ndayiwaliza.

Nthawi itafika 2 : 00 am , ndinadzidzumuka , koma nkazi wanga pa bed panalibepo .
Nditagwila pillow wake , ndinapeza ring yokha ili poteropo.

Ndinayimilira kuyamba kupita kubafa , kenako ndinakumana naye .
Atandiona anadabwa, nkhope yake sinali ngati nkazi yemwe ndamukwatila uja .

Kodi muli inuyo mukanatani mutaona kuti nkazi wanu akuvula ring pakati pausiku?

Ikupitilirabe by Grace 2 sadzu

Omwe taonela . Kodi pachithunzipa pali ndani ndi ndani.Nanga chimachitika ndichani pamenepa.
26/09/2026

Omwe taonela .

Kodi pachithunzipa pali ndani ndi ndani.

Nanga chimachitika ndichani pamenepa.

Part 10 yaponyedwa , kodi yakupezanu ?
26/09/2026

Part 10 yaponyedwa , kodi yakupezanu ?

Address

Cape Town

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Grace 2 sadzu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Grace 2 sadzu:

Shortcuts

Share

Category