Khwenye dizzy mw

Khwenye dizzy mw Yao king nde ifeyo

25/07/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Philoz Philoz, Samuel Pantonial Legumbres, Md Askar Ali, Maya Das Das, Adegboola Ibrahim, Manisha Jaisi, Dipen Basumatary, Ocs WA Laikipia, Mario Paguia, Gundo Phelix, Forto Analyn, Karima Hasan, Sunday Odunlayo, Sahadev Sa, Hussain Basa Khan, Akhwenyani Aja Ndifeyo

22/07/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Philoz Philoz, Samuel Pantonial Legumbres, Md Askar Ali, Maya Das Das, Adegboola Ibrahim, Manisha Jaisi, Dipen Basumatary, Ocs WA Laikipia, Mario Paguia, Gundo Phelix, Forto Analyn, Karima Hasan, Sunday Odunlayo, Sahadev Sa, Akhwenyani Aja Ndifeyo

16/07/2026

Wawa Malawi 🤣🤣🤣

16/07/2026

16/07/2026
16/07/2026

Tipaseni mission tikubwereserani komwe muliko ma boxer komaso ma bra

AFUKULA NDIKUBA THUPI LA KHANDA LOBADWA KUMENE KU DOWA. Anthu okhala m'mudzi wa Kachulu m'dera la Mfumu Yaikulu Chakhaza...
14/07/2026

AFUKULA NDIKUBA THUPI LA KHANDA LOBADWA KUMENE KU DOWA.

Anthu okhala m'mudzi wa Kachulu m'dera la Mfumu Yaikulu Chakhaza m'boma la Dowa, adzidzimuka atapeza kuti manda a khanda lina afukulidwa ndipo thupi lake labedwa.

Izi zachitika sabata latha pamene amayi omwe amapita kuminda anaona kuti mandawo afukulidwa ndipo anauza anthu ena am'mudzimo.

Anthu atapita kumandako anatsimikiza kuti thupi la khandalo, lomwe linaikidwa m'manda Lolemba pa 6july.

Pakadali pano, apolisi ayamba kufufuza kuti adziwe ndi kumanga anthu omwe akukhudzidwa ndi kufukula ndi kuba thupi la khandalo.

Anthunu ufititu uwu zanu azilira kuti mtembo wa mwana wake wabedwa😭💔 dizzy mw

Address

Khwenyefundo@gmail. Com
Blantyre
KHWENYANI

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Khwenye dizzy mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category