Ubale Wa Amalawi Pa Theba

Ubale Wa Amalawi Pa Theba Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ubale Wa Amalawi Pa Theba, Grocers, Boksburg, Johannesburg.

18/10/2024
27/09/2024

AMUNA

Oyimba, Waxy Kay, wati anthu omutsatira asadabwe ndi mmene akuimbira masiku ano pamene wasiya kuimba nyimbo za chamba cha Hipop.

Mnyamatayu yemwe dzina lake lenileni ndi Wonderful Kapenga, wayankhula izi lero pamene watulutsa nyimbo yotchedwa "Bwera" yomwe ili mu chamba Cha Afropop.

"Panopa kayimbidwe kanga kasintha ndipo ndikufuna ndiziyimba nyimbo zachikulu.Izi zachinyamata kwambilizi ndidzipumira kaye chifukwa ndimaona kuti kulibe phindu leni leni", iye watero.

Nyimbo yatsopanoyi kanema wake wajambulidwa ndi Staffa wa ku Bangwe pamene yomvera (Audio) wajambula ndi Swibzy wa mdziko la South Africa.
Mu nyimboyi, Waxy akuyamikira mtsikana komanso kumulimbitsa mtima kuti wafika pa nkhani za chikondi

Address

Boksburg
Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ubale Wa Amalawi Pa Theba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category