Thocco maction Banda

Thocco maction Banda My name is thocco maction Banda

joz ikukoma zaka zambuyomu
18/06/2026

joz ikukoma zaka zambuyomu

dolo wa wina wake
18/06/2026

dolo wa wina wake

4 years nditapota time iyi ndili nyamata
18/06/2026

4 years nditapota time iyi ndili nyamata

4 years ndikuumwatu paden time imeneyo sakukonda kumikuku
18/06/2026

4 years ndikuumwatu paden time imeneyo sakukonda kumikuku

koma nyengo iyiyi ndikudya ndalama eeeee Pano ndimachenji
18/06/2026

koma nyengo iyiyi ndikudya ndalama eeeee Pano ndimachenji

4 years inetu mowa ndiye kudya kwanga
18/06/2026

4 years inetu mowa ndiye kudya kwanga

three years
18/06/2026

three years

17/06/2026

Wina andibwelekeko sate sauzande kwacha ngati Pali twent andipase kuti asale ndingongole yanga ya ten sauzande 🫪

17/06/2026

Aliyense andiyakhe Kodi akazanuwo munawakonda chifukwa choti ndiokongola kapena makhalalidwe awo kapena ali ndalama nanga amunanuwo munawakonda chifukwa ngooneka bwino Kapena ndalama or makhalidwe awo lero ndiziwe ndiyakheni aliyense payekha payekha

abwatikeni nalo bac asazakuphweketseni
16/06/2026

abwatikeni nalo bac asazakuphweketseni

Address

15 Glencoe Road
Johannesburg

Telephone

+27634752198

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Thocco maction Banda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share